132
Created on By webadmin

Grade 7 Cinyanja 2017

1 / 48

Izi ndi .... za akulu anga.

2 / 48

Kamwana ka nkhumba .... gwera mu madzi.

3 / 48

Dailesi anagula cigalimoto .... yera.

4 / 48

Tisiyane ali ndi cimwana ....

5 / 48

Manzunzo wabvala kabudula ....

6 / 48

Gulu la mpira la dziko la Zambia .... mpikisano dzulo.

7 / 48

Atate anamanga .... ya mtedza.

8 / 48

Ife takwera galimoto lofiira .... ku Lusaka

9 / 48

..... kuti anali mtsikana yekha pakati pa anyamata, anakhoza mayeso.

10 / 48

Zebedia wapita ukafula .... kutheng

11 / 48

Agogo ndi .... apita pamodzi kumunda.

12 / 48

Wanyamula nkhwangwa .... phewa

13 / 48

Cipatso camalalanje ndi ....

14 / 48

Tacedwa kusukulu lero cifukwa timayenda ....

15 / 48

CIGAWO CACIWIRI
Cigawo ici ciri ndi mbali ziwiri .Mbali yoyamba iri ndi ziganizo zimene ziri mucindunji
ndi mcisandunji(direct and indirect speech) Mbali yaciwiri iri ndi Mafunso pa
zopumira. Yankhani mafunso kulingana ndi malangizo opezeka pambali iri yonse.
Cindunji ndi cisandunji (direct and indirect speech) sankhani ziganizo zimene
zalembedwa moyenera mwaziganizo zopezeka pa mafunso 16 ndi 17.

“Bwera udzadye nsima,” anatero Dolika kuuza mwana wake.

16 / 48

Munthu wanjala anapempha cakudya nati, “ .... ”

17 / 48

 CIGAWO CACIWIRI
ZOPUMIRA
Malangizo
M‟cigawo ici, funso lirilonse liri ndi ciganizo comwe sicinaikidwe zopumira. M‟malo
onse amene mufunika zopumirazi mwaikidwa manambala. Munsi mwa ganizo
lirilonse mudzapezamo njira yosonyezera kaikidwe ka zopumira m‟malo muli
manambala muja.
Citsanzo: Amai andipatsa mpeni (1) nkhwangwa (2) khasu ndi mpini (3) ndipita
nazo kumunda (4)
1 2 3 4
A ! , ; .
B , ; . .
C , , . .
D . . , .
Yankho „C‟ ndilo loyenera.
Tsopano pakuyankha funso papepala lanu lamayankho, makunaphimba mkabokosi
momwe muli limbo „C‟ motere.
Tsopano yankhani mafunso otsatira:

Aa (1) mwana uyu usowa ulemu (2) kodi ndiwe mwana wayani (3) ndifuna

18 / 48

Pamene Mwatha anapita kumsika (1) anagula mkaka (2) Batala ndi cinkhwa
(3) anagulanso nsomba (4)

19 / 48

Ndani amene ali kupanga phokoso (1) sadziwa kuti alikudzitayira nthawi (2)
muululeni kuti ndithane naye (3) ngati simutero nonsenu mudzalangidwa

(4)
1 2 3 4
A ! ? ? .
B , , ? ,
C ? ? . .
D ? . . !

CIGAWO CACITATU
Malangizo
M‟cigawo ici, funso lirilonse liri ndi ziganizo zinai zimene ziri ndi manambala
osaikidwa mu mndandanda wabwino. Ikani ziganizo izi mu m‟ndandanda wa
dongosolo labwino kuti zonenedwa zonse zikhale zomveka.
Werengani ziganizo zonse mosamala ndi kusankha njira yolongosoka motsatira
manambala kuti zikhale mudongosolo lomveka bwino.
Citsanzo: 1 kodi ndiwe munthu wa mtundu wanji
2 sitidzayenda nawenso kuyambira lero
3 wosafuna kudzisamalira
4 umangoticititsa manyazi pagulu la atsikana
A 4 3 1 2
B 3 2 4 1
C 1 3 4 2
D 2 4 3 1
Yankho “C” ndilo lolongosoka mu mumndandanda. Nkhani yonse iyenera kukhala
tere:

1 kodi ndiwe munthu wa mtundu wanji
3 wosafuna kudzisamalira
4 umangoticititsa manyazi pagulu la atsikana
2 sitidzayenda nawenso kuyambira lero

20 / 48

1 Patapita zaka zambiri, ukwati unatha ndipo anabvutika.
2 Makolo ake anayesetsa kumdandaulira kuti apitirize sukulu.
3 Lute anatenga mimba ali wocepa.
4 Koma iye sanawamvere mpang‟ono ponse.

21 / 48

1 Ng‟ombe za amfumu zinasowa pa mudzi.
2 Anazikusira kwa amfumu.
3 Anthu anayesetsa kufuna-funa koma sanazipeze.
4 M‟nyamata wina wamisala anali kukhala mthengo anaziona ng‟ombezo

22 / 48

1 Ndaitanitsa ng‟ombe zokagaula kumunda.
2 Bwinolake tidzabzala mbeu.
3 Pambuyo pogaula tidzagampha mayenje.
4 Ndipo tidzapalirira mbeuzo zitamera.

23 / 48

1 Anapita kucimemezo ndi galimoto lake.
2 Yosefe anali mwana wodalirika.
3 Kotero anacedwa kufika kumsonkhano.
4 Galimoto lakero linaonongeka m‟njira.

24 / 48

CIGAWO CACINAI

Malangizo
Mcigawo ici, mudzayesedwa ngati mungathe kudziwa matanthauzo a mau, madera a
ziganizo kapena ziganizo zomwe. Munsi mwafunso lirilonse muli mayankho anai.
Yankho limodzi cabe ndilo lopambana ena onse. Phimbani yankho mwasankha
monga mwasonyezedwa pansipa.
Citsanzo: Tikati Belita wapsa mtima ndiko kuti ....

A anatentha mtima.
B mtima wake unali pamoto.
C mtima wake unapsa ndi moto.
D wakalipa kwambiri.

Yankho “D” ndilo loyenera.
Tsopano yankhani mafunso awa:

 Liu lakuti Tonde litanthauza kuti

25 / 48

Mbava siifunika pamudzi. Liu lakuti mbava litanthauza ....

26 / 48

Abanda ndi a cikumbe. Liu lakuti cikumbe litanthauza kuti ....

27 / 48

Amfumu Mungwala anakondwera pamene nyenyezi yawo inabwera. Liu loti nyenyezi mciganizo litanthauza .....

28 / 48

Kodi mukumvanji pa mau oti, „anamva za m‟maluwa‟.

29 / 48

Tikambenji ndi fisi, sangathe kuyenda yekha usiku. Ciganizo ici citanthauza wa ....

30 / 48

Ciganizo cakuti, „Jeremiya athamanga monga mphenzi.‟ Citanthauza ....

31 / 48

Mwambi wakuti „mlendo ndi mame‟ utanthauza ciani? Mlendo ....

32 / 48

Dzulo aphunzi anapha .... m‟kalasi

33 / 48

Amai ..... pamene mwana wao Tikambenji anapambana mayeso a giredi 7.

34 / 48

CIGAWO CACISANU
MALANGIZO
Munsimu muli mau ndi ziganizo zolembedwa m‟cingerezi sankhani yankho limene liri
ndi liu kapena ciganizo cimene catembenuzidwa m‟Cinyanja comveka bwino, mwa
ziganizo zinai zapatsidwazi.

Liu lakuti, “surprised” m‟cingerezi ndi .... m‟cinyanja.

35 / 48

Liu lakuti “axe” mcingerezi ndi .... mcinyanja.

36 / 48

Ciganizo cakuti, “I am a leader of a church” m‟cingerezi ndi  m‟cinyanja.

37 / 48

Ciganizo cakuti, “mothers love their children” m‟cingerezi ndi .... m‟cinyanja.

38 / 48

Ciganizo cakuti, “I like reading books” m‟cingerezi ndi .... m‟cinyanja

39 / 48

CIGAWO CACISANU NDI CIMODZ

Werengani nkhani iyi ndipo muyankhe mafunso otsatira.

Nthawi yoyembekezera zotuluka za m‟mayeso imakhala yobvuta kwambiri ku
aphunzi. Anyamata ndi atsikana ena amatengako mbali kumakhalidwe oipa monga
ya kumwa mowa ndi kusuta fodya.
Koma mkhalidwe wa Msaode sunali wotero. Iyeyu anali kukonda kupita
kumunda kukalima pamodzi ndi makolo ake. Motero, makolo ndi anansi ake,
anamkonda
kwambiri
mwana
wao.
Comukondera
cinali
cikhalidwe
cakeco
conyadiritsa banjalo.
Zotuluka m‟mayeso zitatuluka, Msaode anali m‟modzi mwa aphunzi amene
anakhoza mayeso. Ici cinasangalatsa aphunzitsi, makolo ndi anansi.
Cifukwa ca ici, aphunzitsi anamupatsa mabuku asanu pamene amai ake
anamuphera nkhuku. Acinansi ena monga agogo ake anamupondera ciponde ndi
kumuwambira nyama ya mbuzi.
Cifukwa ca mphatsozi, aja amene anajomba m‟mayeso ao anamuda m‟nzao.
Iwo anali kuti akamuona; anali kumthawa. Mwinanso anali kumulankhulira kukhosi.
Izi zinakwinyiriritsa Msaode cifukwa anasowa abwenzi wosewera nao.
Mukupita kwa nthawi zinthu zinasintha. Aja onse anali kumuthawa ndinso
kumulankhulira kukhosi anadzitsutsa. Kenaka anayamba kufendera ndi kusewerera
limodzi ndi Msaode.
Tsopano yankhani mafunso yotsatira awa

40 / 48

Liu loti, „mphunzi‟ litanthauza ....

41 / 48

Ndi mphatso yotani imene amai ake Msaode anapatsa mwana wao.

42 / 48

Ciganizo cakuti „kusuta fodya‟ citanthauza ....

43 / 48

Ciganizo cakuti, „anali kumthawa,‟ citanthanza ....

44 / 48

Kodi ndi ana otani amene asangalatsa makolo ao?

45 / 48

Ciganizo cakuti, „amene anajomba m‟mayeso‟ citanthauza.

46 / 48

Kodi ndi phunziro lotani limene tingatengemo munkhani imene tawerenga?

47 / 48

Sankhani mutu woyenera wa nkhani imene mwawerenga.

48 / 48

Msaode anasangalatsa makolo ake cifukwa ca .... cake.

Your score is

The average score is 28%

0%